Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 3:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinauza Yoswa muja, ndi kuti, Maso ako anapenya zonse Yehova Mulungu wanu anawacitira mafumu awa awiri; momwemo Yehova adzacitira maufumu onse kumene muolokerako.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 3

Onani Deuteronomo 3:21 nkhani