Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 23:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukawindira Yehova Mulungu wanu cowinda, musamacedwa kucicita; popeza Yehova Mulungu wanu adzakufunsani za ici ndithu ndipo mukadacimwako.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 23

Onani Deuteronomo 23:21 nkhani