Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 23:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukongoletse mlendo mopindulitsa; koma mbale wanu musamamkongoletsa mopindulitsa, kuti Yehova Mulungu wanu akudalitseni mwa zonse muzigwira ndi dzanja lanu, m'dziko limene mulowamo kulilandira.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 23

Onani Deuteronomo 23:20 nkhani