Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 20:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene mumangira tsasa mudzi masiku ambiri, pouthirira nkhondo kuugwira, usamaononga mitengo yace ndi kuitema ndi nkhwangwa; pakuti ukadyeko, osailikha; pakuti mtengo wa m'munda ndiwo munthu kodi kuti uumangire tsasa?

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 20

Onani Deuteronomo 20:19 nkhani