Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 16:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muziphera Yehova Mulungu wanu nsembe ya Paskha, ya nkhosa ndi ya ng'ombe, m'malo amene Yehova adzasankha kukhalitsamo dzina lace.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16

Onani Deuteronomo 16:2 nkhani