Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 16:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musamadyera nayo mkaye wa cotupitsa; masiku asanu ndi awiri mudyere nayo mkate wopanda cotupitsa, ndiwo mkate wa cizunziko popeza munaturuka m'dziko la Aigupto mofulumira; kuti inu kumbukile tsiku loturuka inu m'dziko la Aigupto masiku onse a moyo wanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16

Onani Deuteronomo 16:3 nkhani