Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 16:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Samalirani mwezi wa Abibu, kuti muzicitira Yehova Mulungu wanu Paskha; popeza m'mwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakuturutsani m'dziko la Aigupto usiku.

2. Ndipo muziphera Yehova Mulungu wanu nsembe ya Paskha, ya nkhosa ndi ya ng'ombe, m'malo amene Yehova adzasankha kukhalitsamo dzina lace.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 16