Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 15:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musamayesa neosautsa, pomlola akucokereni waufulu; popeza anakugwirirani nchito zaka zisanu ndi cimodzi monga wolipidwa wakulandira cowirikiza; potero Yehova Mulungu wanu adzakudalitsani m'zonse muzicita.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 15

Onani Deuteronomo 15:18 nkhani