Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 15:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo muzitenga lisungulo, ndi kulipisa m'khutu mwace, kulikanikiza ndi citseko, ndipo adzakhala kapolo wanu kosalekeza. Muzicitanso momwemo ndi adzakazi anu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 15

Onani Deuteronomo 15:17 nkhani