Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 13:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mneneriyo, kapena wolota malotoyo, mumuphe; popeza ananena cosiyanitsa ndi Yehova Mulungu wanu, amene anakuturutsani m'dziko la Aigupto, nakuombolani m'nyumba ya akapolo; kuti akuceteni mutaye njira imene Yehova Mulungu wanu anakulamulirani muziyendamo. Potero muzicotsa coipaco pakati pa inu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 13

Onani Deuteronomo 13:5 nkhani