Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 13:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Muziyenda kutsata Yehova Mulungu wanu, ndi kumuopa, ndi kusunga malamulo ace, ndi kumvera mau ace, ndi kumtumikira iye, ndi kummamatira.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 13

Onani Deuteronomo 13:4 nkhani