Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 12:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nimugumule maguwa ao a nsembe, ndi kuphwanya zoimiritsa zao, ndi kutentha zifanizo zao, ndi kulikha mafano osema a milungu yao; ndipo muononge dzina lao licoke m'malomo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12

Onani Deuteronomo 12:3 nkhani