Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 12:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo padzakhala malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankha kukhalitsako dzina lace, kumeneko muzibwera nazo zonse ndikuuzanizi; nsembe zanu zopsereza, ndi nsembe zanu zophera, magawo anu onse a magawo khumi, ndi nsembe yokweza dzanja lanu, ndi zowinda zanu zosankhika zimene muzilonjezera Yehova.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12

Onani Deuteronomo 12:11 nkhani