Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 12:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mudzakondwera pamaso pa Yehova Mulungu wanu, inu ndi ana anu amuna, ndi ana anu akazi, ndi anchito anu amuna, ndi anchito anu akazi, ndi Mlevi ali m'midzi mwanu, popeza alibe gawo kapena colowa pamodzi ndi inu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 12

Onani Deuteronomo 12:12 nkhani