Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 1:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinauza oweruza anu muja, ndi kuti, Mverani milandu ya pakati pa abale anu, ndi kuweruza kolungama pakati pa munthu ndi mbale wace, ndi mlendo wokhala naye.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1

Onani Deuteronomo 1:16 nkhani