Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 1:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musamasamalira munthu poweruza mlandu; ang'ono ndi akuru muwamvere m'modzimodzi; musamaopa nkhope ya munthu; popeza ciweruzo nca Mulungu; ndipo mlandu ukakulakani mubwere nao kwa ine, ndidzaumva.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1

Onani Deuteronomo 1:17 nkhani