Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 1:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero ndinatenga akuru a mapfuko anu, amuna anzeru, ndi odziwika, ndi kuwaika akhale akuru anu, atsogoleri a zikwi, ndi atsogoleri a mazana, ndi atsogoleri a makumi asanu, ndi atsogoleri a makumi, ndi akapitao, a mapfuko anu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1

Onani Deuteronomo 1:15 nkhani