Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 8:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndinamva wina woyera, alikunena; ndi wina woyera anati kwa iye uja wanenayo, Masomphenya a nsembe yopsereza yacikhalire, ndi colakwa cakupululutsa ca kupereka malo opatulika ndi khamulo ziponderezedwe, adzakhala mpaka liti?

Werengani mutu wathunthu Danieli 8

Onani Danieli 8:13 nkhani