Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 8:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo khamulo linaperekedwa kwa iyo, pamodzi ndi nsembe yopsereza yacikhalire mwa kulakwa kwace, nigwetsa pansi coonadi, nicita cifuniro cace, nikuzika.

Werengani mutu wathunthu Danieli 8

Onani Danieli 8:12 nkhani