Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 7:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pambuyo pace ndinaona m'masomphenya a usiku, ndi kuona cirombo cacinai, coopsa ndi cocititsa mantha, ndi camphamvu coposa, cinali nao mano akuru acitsulo, cinalusa ndi kuphwanya ndi kupondereza cotsala ndi mapazi ace; cinasiyana ndi zirombo zonse zidacitsogolera; ndipo cinali ndi nyanga khumi.

Werengani mutu wathunthu Danieli 7

Onani Danieli 7:7 nkhani