Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 7:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pambuyo pace ndinapenya ndi kuona cina ngati nyalugwe, cinali nao mapiko anai a nkhuku pamsana pace, ciromboco cinali nayonso mitu inai, nicinapatsidwa ulamuliro.

Werengani mutu wathunthu Danieli 7

Onani Danieli 7:6 nkhani