Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

popeza m'Danieli yemweyo, amene mfumu adamucha Belitsazara, mudapezeka mzimu wopambana, ndi cidziwitso, ndi luntha, kumasulira maloto ndi kutanthauzira mau ophiphiritsa, ndi kumasula mfundo. Amuitane Danieli tsono, iye adzafotokozera kumasuliraku.

Werengani mutu wathunthu Danieli 5

Onani Danieli 5:12 nkhani