Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 5:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pali munthu m'ufumu mwanu mwa iye muli mzimu wa milungu yoyera; ndipo masiku a atate wanu munapezeka mwa iye kuunika, ndi luntha, ndi nzeru, ngati nzeru ya milungu; ndipo mfumu Nebukadinezara atate wanu, inde mfumu atate wanu anamuika akhale mkuru wa alembi, openda, Akasidi, ndi alauli;

Werengani mutu wathunthu Danieli 5

Onani Danieli 5:11 nkhani