Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 4:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Danieli, dzina lace ndiye Belitsazara anadabwa nthawi, namsautsa maganizo ace. Mfumu inayankha, niti, Belitsazara, lisakusautse lotoli, kapena kumasulira kwace. Belitsazara anayankha, nati, Mbuye wanga, lotoli likadakhala la iwo akudana nanu, ndi kumasulira kwace kwa iwo akuutsana nanu.

Werengani mutu wathunthu Danieli 4

Onani Danieli 4:19 nkhani