Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 4:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Loto ili ndinaliona ine mfumu Nebukadinezara; ndipo iwe, Belitsazara, undifotokozere kumasulira kwace, popeza anzeru onse a m'ufumu wanga sakhoza kundidziwitsa kumasulira kwace; koma iwe ukhoza, popeza mwa iwe muli mzimu wa milungu yoyera.

Werengani mutu wathunthu Danieli 4

Onani Danieli 4:18 nkhani