Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 4:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Citsutso ici adacilamulira amithenga oyerawo, anacifunsa, nacinena, kuti amoyo adziwe kuti Wam'mwambamwamba alamulira m'ufumu wa anthu, naupereka kwa ali yense Iye afuna, nauutsira wolubukira anthu.

Werengani mutu wathunthu Danieli 4

Onani Danieli 4:17 nkhani