Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Danieli 2:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akasidi anayankha pamaso pa mfumu, nati, Palibe munthu pa dziko lapansi wokhoza kuulula mlandu wa mfumu; cifukwa cace palibe mfumu, mkuru, kapena wolamulira, wafunsira cinthu cotere kwa mlembi, kapena wopenduza, kapena Akasidi ali onse.

Werengani mutu wathunthu Danieli 2

Onani Danieli 2:10 nkhani