Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 7:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tsono udzatero kwa mtumiki wanga Davide, Atero Yehova wa makamu, Ndinakucotsa kubusako kumene unalikutsata nkhosa kuti udzakhale mfumu ya anthu anga, ndiwo Israyeli,

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7

Onani 2 Samueli 7:8 nkhani