Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 7:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

monga kuyambira tsiku lija ndinalamulira oweruza kuyang'anira anthu anga Israyeli; ndipo ndidzakupumulitsa kwa adani ako onse. Yehova akuuzanso kuti Yehova adzakumangira banja.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7

Onani 2 Samueli 7:11 nkhani