Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 7:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzaikira anthu anga Israyeli malo, ndi kuwaoka kuti akakhale m'malo ao a iwo okha, osasunthikanso. Ndipo anthu a mphulupulu sadzawabvutanso, monga poyamba paja,

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 7

Onani 2 Samueli 7:10 nkhani