Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 6:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ananyamuka, namuka nao anthu onse anali naye, nacokera ku Baale-Yuda natengako likasa la Mulungu, limene amachula nalo Dzinalo Dzina la Yehova wa makamu, wokhala pakati pa Akerubi.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 6

Onani 2 Samueli 6:2 nkhani