Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 6:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo ananyamulira likasa la Mulungu pa gareta watsopano, ataliturutsa m'nyumba ya Abinadabu, iri pacitunda, ndipo Uza ndi Ahio ana a Abinadabu anayendetsa ng'ombe za pa gareta watsopanoyo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 6

Onani 2 Samueli 6:3 nkhani