Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 5:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco akuru onse a Israyeli anadza kwa mfumu ku Hebroni; ndipo mfumu Davide anapangana nao pangano ku Hebroni pamaso pa Yehova; ndipo anamdzoza Davide mfumu ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 5

Onani 2 Samueli 5:3 nkhani