Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 5:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anafika ku Baalaperazimu, nawakantha kumeneko Davideyo; nati, Yehova wathyola adani anga pamaso panga ngati madzi okamulira. Cifukwa cace analicha dzina la malowo Baalaperazimu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 5

Onani 2 Samueli 5:20 nkhani