Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 4:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anabwera nao mutu wa Isiboseti kwa Davide ku Hebroni, nanena ndi mfumu, Taonani mutu wa Isiboseti mwana wa Sauli, mdani wanu amene anafuna moyo wanu; Yehova anabwezerera cilango mbuye wanga mfumu lero lino kwa Sauli ndi mbeu yace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 4

Onani 2 Samueli 4:8 nkhani