Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 4:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma polowa iwo m'nyumbamo iye ali cigonere pakama pace m'cipindamo, anamkantha, namupha namdula mutu wace, nautenga namuka njira ya kucidikha usiku wonse,

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 4

Onani 2 Samueli 4:7 nkhani