Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 3:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, anyamata a Davide ndi Yoabu anabwera kucokera ku nkhondo yobvumbulukira, nakhala nazo zofunkha zambiri. Koma Abineri sanali ku Hebroni kwa Davide, cifukwa adalawirana naye ndipo adamuka mumtendere.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3

Onani 2 Samueli 3:22 nkhani