Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 3:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo Abined anati kwa Davide, Ndidzanyamuka ndi kupita ndi kusonkhanitsira mfumu mbuye wanga Aisrayeli onse, kuti adzapangane nanu pangano, ndi kuti mukhale mfumu pa zonse mtima wanu uzikhumba. Comweco Davide analawirana ndi Abineri, namuka iye mumtendere.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3

Onani 2 Samueli 3:21 nkhani