Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 24:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco Gadi anafika kwa Davide, namuuza, nanena naye, Kodi zikugwereni m'dziko mwanu zaka zisanu ndi ziwiri za njala? Kapena muthawe adani anu akukupitikitsani miyezi itatu? kapena m'dziko mwanu mukhale mliri masiku atatu? Cenjerani tsono ndi kulingalira bwino mau amene ine ndibwere nao kwa wonditumayo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:13 nkhani