Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 23:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Maina a ngwazi Davide anali nazo ndiwo: Josebu-basebete Mtakemoni, mkuru wa akazembe; ameneyu ndiye Adino M-ezni wolimbana ndi mazana atatu ophedwa nthawi imodzi.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 23

Onani 2 Samueli 23:8 nkhani