Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 23:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wotsatana naye Eleazeri mwana wa Dodai mwana wa M-akohi, mmodzi wa ngwazi zitatu zokhala ndi Davide pamene iwo anatonza Afilisti osonkhanidwa kunkhondo kumeneko, atacoka Aisrayeli;

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 23

Onani 2 Samueli 23:9 nkhani