Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 22:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Davide analankhula kwa Yehova mau a nyimbo iyi tsikuli Yehova anampulumutsa m'dzanja la adani ace onse, ndi m'dzanja la Sauli.

2. Ndipo anati:-Yehova ndiye thanthwe langa, ndi ngaka yanga, ndi mpulumutsi wanga, wangadi;

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 22