Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 22:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide analankhula kwa Yehova mau a nyimbo iyi tsikuli Yehova anampulumutsa m'dzanja la adani ace onse, ndi m'dzanja la Sauli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 22

Onani 2 Samueli 22:1 nkhani