Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 20:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mranduwo soli wotere ai, koma munthu wa ku dziko lamapiri la Efraimu, dzina lace ndiye Seba mwana wa Bikri, anakweza dzanja lace pa mfumu Davide; mpereke iye yekha ndipo ndidzacoka kumudzi kuno. Ndipo mkaziyo anati kwa Yoabu, Onani tidzakuponyerani mutu wace kutumphitsa Gnga.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20

Onani 2 Samueli 20:21 nkhani