Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 20:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo mkaziyo anapita kwa anthu onse mwa nzeru yace. Ndipo iwo anadula mutu wa Seba mwana wa Bikri, nauponya kunja kwa Yoabu. Ndipo analiza Gpenga, nabalalika kucoka pamudzipo, munthu yense kumka ku hema wace. Ndipo Yoabu anabwerera kumka ku Yerusalemu kwa mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20

Onani 2 Samueli 20:22 nkhani