Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu onse anaoloka Yordano, ndi mfumu yomwe inaoloka; ndipo mfumuyo Inapsompsona Barizilai nimdalitsa; ndipo iye anabwerera kunka kumalo kwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:39 nkhani