Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inayankha, Cimamu adzaoloka nane, ndipo ndidzamcitira cimene cikukomereni; ndipo ciri conse mukadzapempha kwa ine ndidzakucitirani inu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:38 nkhani