Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco mfumu inaoloka nifika ku Giligala, ndi Cimamu anaoloka naye, ndipo anthu onse a Yuda adaolotsa mfumu, ndiponso gawo lina la anthu a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:40 nkhani