Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 19:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mulole mnyamata wanu ndibwererenso, kuti ndikamwalire m'mudzi wanga ku manda a atate wanga ndi mai wanga. Koma suyu, Cimamu mnyamata wanu, iye aoloke pamodzi ndi mbuye wanga mfumu, ndipo mumcitire cimene cikukomerani.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19

Onani 2 Samueli 19:37 nkhani