Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 17:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tsono mutumize msanga nimuuze Davide kuti, Musagona usiku uno pa madooko a kucipululu, koma muoloke ndithu, kuti mfumu ingamezedwe ndi anthu onse amene ali naye.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 17

Onani 2 Samueli 17:16 nkhani